Machitidwe 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Paulo podziteteza anati: “Ine sindinachimwire Chilamulo cha Ayuda, kapena kachisi,+ kapena Kaisara.”+
8 Koma Paulo podziteteza anati: “Ine sindinachimwire Chilamulo cha Ayuda, kapena kachisi,+ kapena Kaisara.”+