Machitidwe 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho pothedwa nzeru ndi mkangano wa nkhani zimenezi, ndinamufunsa ngati akufuna kupita ku Yerusalemu kuti nkhanizi zikaweruzidwire kumeneko.+
20 Choncho pothedwa nzeru ndi mkangano wa nkhani zimenezi, ndinamufunsa ngati akufuna kupita ku Yerusalemu kuti nkhanizi zikaweruzidwire kumeneko.+