Machitidwe 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mwamuna ameneyu anali kumvetsera pamene Paulo anali kulankhula. Ndiyeno Paulo atamuyang’anitsitsa anaona kuti ali ndi chikhulupiriro+ ndipo angathe kuchiritsidwa.
9 Mwamuna ameneyu anali kumvetsera pamene Paulo anali kulankhula. Ndiyeno Paulo atamuyang’anitsitsa anaona kuti ali ndi chikhulupiriro+ ndipo angathe kuchiritsidwa.