Machitidwe 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamapeto pake, titalowa mu Roma, Paulo analoledwa+ kumakhala yekha ndi msilikali womulondera.