1 Yohane 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ana anga okondedwa, ndikukulemberani zinthu izi kuti musachite tchimo.+ Komabe, wina akachita tchimo, tili ndi mthandizi+ wolungama, Yesu Khristu, amene ali ndi Atate.+
2 Ana anga okondedwa, ndikukulemberani zinthu izi kuti musachite tchimo.+ Komabe, wina akachita tchimo, tili ndi mthandizi+ wolungama, Yesu Khristu, amene ali ndi Atate.+