Machitidwe 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamene atumwi ku Yerusalemu anamva kuti Asamariya alandira mawu a Mulungu,+ anawatumizira Petulo ndi Yohane.
14 Pamene atumwi ku Yerusalemu anamva kuti Asamariya alandira mawu a Mulungu,+ anawatumizira Petulo ndi Yohane.