Yesaya 28:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 anthu amene wawauza kuti: “Awa ndiye malo opumira. Pumitsani munthu wotopa. Amenewa ndiwo malo ampumulo,” koma amene sanafune kumva.+
12 anthu amene wawauza kuti: “Awa ndiye malo opumira. Pumitsani munthu wotopa. Amenewa ndiwo malo ampumulo,” koma amene sanafune kumva.+