Machitidwe 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma mobisa iye anapatula zina mwa ndalamazo n’kusunga, mkazi wakenso anadziwa zimenezo. Ndiyeno anabweretsa zotsalazo n’kudzazipereka kwa atumwi.+
2 Koma mobisa iye anapatula zina mwa ndalamazo n’kusunga, mkazi wakenso anadziwa zimenezo. Ndiyeno anabweretsa zotsalazo n’kudzazipereka kwa atumwi.+