Deuteronomo 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uzisunga mawu a pakamwa pako+ ndipo uzikwaniritsa lonjezo limene unapereka kwa Yehova Mulungu wako monga nsembe yaufulu. Uzichita zimenezi chifukwa unalonjeza ndi pakamwa pako.+
23 Uzisunga mawu a pakamwa pako+ ndipo uzikwaniritsa lonjezo limene unapereka kwa Yehova Mulungu wako monga nsembe yaufulu. Uzichita zimenezi chifukwa unalonjeza ndi pakamwa pako.+