1 Petulo 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti ino ndiyo nthawi yoikidwiratu yakuti chiweruzo chiyambe, ndipo chiyambira panyumba ya Mulungu.+ Tsopano ngati chikuyambira pa ife,+ ndiye mapeto a anthu osamvera uthenga wabwino wa Mulungu adzakhala otani?+
17 Pakuti ino ndiyo nthawi yoikidwiratu yakuti chiweruzo chiyambe, ndipo chiyambira panyumba ya Mulungu.+ Tsopano ngati chikuyambira pa ife,+ ndiye mapeto a anthu osamvera uthenga wabwino wa Mulungu adzakhala otani?+