Yohane 6:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Simoni Petulo+ anayankha kuti: “Ambuye, tingapitenso kwa ndani?+ Inu ndi amene muli ndi mawu amoyo wosatha.+
68 Simoni Petulo+ anayankha kuti: “Ambuye, tingapitenso kwa ndani?+ Inu ndi amene muli ndi mawu amoyo wosatha.+