Machitidwe 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsiku lotsatira, olamulira ndi akulu ndiponso alembi anasonkhana pamodzi mu Yerusalemu.+