Machitidwe 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Mulungu anamuukitsa+ kwa akufa mwa kumasula zopweteka za imfa,+ chifukwa zinali zosatheka kuti imfa ipitirize kumugwira mwamphamvu.+ Machitidwe 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa.+
24 Koma Mulungu anamuukitsa+ kwa akufa mwa kumasula zopweteka za imfa,+ chifukwa zinali zosatheka kuti imfa ipitirize kumugwira mwamphamvu.+