Machitidwe 2:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iye anakwezedwa kudzanja lamanja la Mulungu+ ndipo analandira mzimu woyera wolonjezedwawo kuchokera kwa Atate.+ Choncho iye watitsanulira mzimu woyera umene mukuuona ndi kuumvawu. Afilipi 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa chifukwa chimenechinso, Mulungu anamukweza n’kumuika pamalo apamwamba.+ Ndipo anamukomera mtima n’kumupatsa dzina loposa lina lililonse.+
33 Iye anakwezedwa kudzanja lamanja la Mulungu+ ndipo analandira mzimu woyera wolonjezedwawo kuchokera kwa Atate.+ Choncho iye watitsanulira mzimu woyera umene mukuuona ndi kuumvawu.
9 Pa chifukwa chimenechinso, Mulungu anamukweza n’kumuika pamalo apamwamba.+ Ndipo anamukomera mtima n’kumupatsa dzina loposa lina lililonse.+