Machitidwe 21:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kodi si iwe Mwiguputo uja amene masiku apitawo unayambitsa chipolowe choukira boma+ ndi kutsogolera zigawenga 4,000 kupita nazo m’chipululu?”
38 Kodi si iwe Mwiguputo uja amene masiku apitawo unayambitsa chipolowe choukira boma+ ndi kutsogolera zigawenga 4,000 kupita nazo m’chipululu?”