Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 2:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Tsiku ndi tsiku anali kusonkhana kukachisi mogwirizana.+ Analinso kuyenderana m’nyumba zawo ndi kudyera limodzi chakudya mosangalala+ ndiponso ndi mtima wofunitsitsa kugawana zinthu.

  • Machitidwe 4:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Atatha kupembedzera, malo amene anasonkhanawo anagwedezeka.+ Pamenepo aliyense wa iwo anadzazidwa ndi mzimu woyera,+ ndipo anayamba kulankhula mawu a Mulungu molimba mtima.+

  • Machitidwe 18:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tsopano Sila+ ndi Timoteyo+ atafika kuchokera ku Makedoniya, Paulo anatanganidwa kwambiri ndi ntchito yolalikira mawu a Mulungu. Iye anali kuchitira umboni kwa Ayuda ndi kuwatsimikizira kuti Yesu ndiyedi Khristu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena