2 Akorinto 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho sitikupitirira malire a gawo lathu, ngati kuti gawolo silikufika kwa inu. Ayi ndithu, pakuti tinayamba ndife kufika kwanuko polengeza uthenga wabwino wonena za Khristu.+
14 Choncho sitikupitirira malire a gawo lathu, ngati kuti gawolo silikufika kwa inu. Ayi ndithu, pakuti tinayamba ndife kufika kwanuko polengeza uthenga wabwino wonena za Khristu.+