Maliko 12:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mwa mzimu woyera,+ Davideyo ananena kuti, ‘Yehova anauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja kufikira nditaika adani ako kunsi kwa mapazi ako.”’+
36 Mwa mzimu woyera,+ Davideyo ananena kuti, ‘Yehova anauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja kufikira nditaika adani ako kunsi kwa mapazi ako.”’+