Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 11:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Pambuyo pake Tera anatenga mwana wake Abulamu, mdzukulu wake+ Loti mwana wa Harana, Sarai+ mpongozi wake, mkazi wa mwana wake Abulamu, ndi kunyamuka kuchoka mumzinda wa Akasidi wa Uri, kupita kudziko la Kanani.+ Kenako, anafika ku Harana+ ndipo anakhala kumeneko.

  • Genesis 15:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Anamuuzanso kuti: “Ine ndine Yehova, amene ndinakuchotsa ku Uri wa kwa Akasidi, kudzakupatsa dzikoli kuti likhale lako.”+

  • Nehemiya 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Inu ndinu Yehova Mulungu woona, amene munasankha Abulamu+ ndi kum’tulutsa ku Uri wa Akasidi+ ndipo munamutcha dzina lakuti Abulahamu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena