Genesis 37:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Abale akewo anachita naye kaduka,+ koma bambo ake anasunga mawuwo.+