Genesis 42:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anapitiriza kuti: “Ine ndamva kuti ku Iguputo kuli tirigu.+ Pitani kumeneko mukatigulire tirigu kuti tikhalebe ndi moyo, tingafe ndi njala.”
2 Anapitiriza kuti: “Ine ndamva kuti ku Iguputo kuli tirigu.+ Pitani kumeneko mukatigulire tirigu kuti tikhalebe ndi moyo, tingafe ndi njala.”