Genesis 45:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Pamenepo Yosefe analephera kudzigwira pamaso pa anthu onse amene anaima pafupi naye.+ Choncho anafuula kuti: “Tulutsani aliyense muno!” Motero, panalibe aliyense amene anali naye pa nthawi imene Yosefe ankadziulula kwa abale ake.+
45 Pamenepo Yosefe analephera kudzigwira pamaso pa anthu onse amene anaima pafupi naye.+ Choncho anafuula kuti: “Tulutsani aliyense muno!” Motero, panalibe aliyense amene anali naye pa nthawi imene Yosefe ankadziulula kwa abale ake.+