Genesis 45:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nkhani inamveka kunyumba kwa Farao kuti: “Abale ake a Yosefe abwera!” Farao ndi atumiki ake anasangalala atamva zimenezo.+
16 Nkhani inamveka kunyumba kwa Farao kuti: “Abale ake a Yosefe abwera!” Farao ndi atumiki ake anasangalala atamva zimenezo.+