Aheberi 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mwa chikhulupiriro, Mose atabadwa, makolo ake anamubisa kwa miyezi itatu,+ chifukwa anaona kuti mwanayo anali wokongola.+ Iwo sanaope lamulo+ la mfumu.
23 Mwa chikhulupiriro, Mose atabadwa, makolo ake anamubisa kwa miyezi itatu,+ chifukwa anaona kuti mwanayo anali wokongola.+ Iwo sanaope lamulo+ la mfumu.