Salimo 69:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Msasa wawo wokhala ndi mpanda ukhale bwinja,+Ndipo m’mahema awo musapezeke munthu wokhalamo.+