Salimo 109:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Masiku a moyo wake akhale ochepa.+Udindo wake monga woyang’anira utengedwe ndi munthu wina.+ 1 Timoteyo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mawu awa ndi oona.+ Ngati munthu aliyense akuyesetsa kuti akhale woyang’anira,+ akufuna ntchito yabwino.
3 Mawu awa ndi oona.+ Ngati munthu aliyense akuyesetsa kuti akhale woyang’anira,+ akufuna ntchito yabwino.