Mateyu 23:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chotero mukudzichitira nokha umboni kuti ndinu ana a anthu amene anapha aneneri.+