Machitidwe 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno anthu amene anabalalika+ chifukwa cha chisautso chimene chinagwera Sitefano anayenda mpaka ku Foinike,+ ku Kupuro+ ndi ku Antiokeya. Ndipo sanali kulalikira mawu kwa wina aliyense koma kwa Ayuda okha.+
19 Ndiyeno anthu amene anabalalika+ chifukwa cha chisautso chimene chinagwera Sitefano anayenda mpaka ku Foinike,+ ku Kupuro+ ndi ku Antiokeya. Ndipo sanali kulalikira mawu kwa wina aliyense koma kwa Ayuda okha.+