Mateyu 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chiritsani odwala,+ ukitsani anthu akufa, yeretsani akhate, tulutsani ziwanda. Munalandira kwaulere, patsani kwaulere.+ Machitidwe 10:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ndipo okhulupirika amene anabwera ndi Petulo, amene anali odulidwa anadabwa, chifukwa mphatso yaulere ya mzimu woyera inalinso kuthiridwa pa anthu a mitundu ina.+
8 Chiritsani odwala,+ ukitsani anthu akufa, yeretsani akhate, tulutsani ziwanda. Munalandira kwaulere, patsani kwaulere.+
45 Ndipo okhulupirika amene anabwera ndi Petulo, amene anali odulidwa anadabwa, chifukwa mphatso yaulere ya mzimu woyera inalinso kuthiridwa pa anthu a mitundu ina.+