Machitidwe 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Petulo ali mkati moganizira za masomphenyawo, mzimu+ unati: “Tamvera! Pali amuna atatu amene akukufuna.
19 Petulo ali mkati moganizira za masomphenyawo, mzimu+ unati: “Tamvera! Pali amuna atatu amene akukufuna.