Yesaya 53:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anapanikizidwa+ ndipo analola kuti asautsidwe,+ koma sanatsegule pakamwa pake. Anatengedwa ngati nkhosa yopita kokaphedwa,+ ndipo mofanana ndi nkhosa yaikazi imene imakhala chete akamaimeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+ 1 Petulo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene anali kunenedwa zachipongwe,+ sanabwezere zachipongwe.+ Pamene anali kuvutika,+ sanawopseze, koma anali kudzipereka kwa iye+ amene amaweruza molungama.
7 Iye anapanikizidwa+ ndipo analola kuti asautsidwe,+ koma sanatsegule pakamwa pake. Anatengedwa ngati nkhosa yopita kokaphedwa,+ ndipo mofanana ndi nkhosa yaikazi imene imakhala chete akamaimeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+
23 Pamene anali kunenedwa zachipongwe,+ sanabwezere zachipongwe.+ Pamene anali kuvutika,+ sanawopseze, koma anali kudzipereka kwa iye+ amene amaweruza molungama.