1 Akorinto 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma pomalizira pake anaonekera kwa ine,+ ngati khanda lobadwa masiku asanakwane.