2 Akorinto 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ku Damasiko, bwanamkubwa wa mfumu Areta anali kulondera mzinda wa Adamasiko kuti andigwire,+