Machitidwe 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munthu ameneyu ndi mlendo kunyumba kwa Simoni wina wofufuta zikopa, amene nyumba yakeyo ili m’mbali mwa nyanja.”+ Machitidwe 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Chotero tumiza anthu ku Yopa, kuti akaitane Simoni wotchedwanso Petulo.+ Munthu ameneyo ndi mlendo m’nyumba ya Simoni wofufuta zikopa, amene amakhala m’mbali mwa nyanja.’+
6 Munthu ameneyu ndi mlendo kunyumba kwa Simoni wina wofufuta zikopa, amene nyumba yakeyo ili m’mbali mwa nyanja.”+
32 Chotero tumiza anthu ku Yopa, kuti akaitane Simoni wotchedwanso Petulo.+ Munthu ameneyo ndi mlendo m’nyumba ya Simoni wofufuta zikopa, amene amakhala m’mbali mwa nyanja.’+