Machitidwe 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano ulendo wathu wa pamadzi wopita ku Italiya utatsimikizika,+ anapereka Paulo ndi akaidi ena m’manja mwa kapitawo wa asilikali dzina lake Yuliyo, wa m’gulu la asilikali la Augusito.
27 Tsopano ulendo wathu wa pamadzi wopita ku Italiya utatsimikizika,+ anapereka Paulo ndi akaidi ena m’manja mwa kapitawo wa asilikali dzina lake Yuliyo, wa m’gulu la asilikali la Augusito.