Machitidwe 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Atatha kupembedzera, malo amene anasonkhanawo anagwedezeka.+ Pamenepo aliyense wa iwo anadzazidwa ndi mzimu woyera,+ ndipo anayamba kulankhula mawu a Mulungu molimba mtima.+ Machitidwe 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iwo anapitadi kumeneko ndipo anawapempherera kuti alandire mzimu woyera.+
31 Atatha kupembedzera, malo amene anasonkhanawo anagwedezeka.+ Pamenepo aliyense wa iwo anadzazidwa ndi mzimu woyera,+ ndipo anayamba kulankhula mawu a Mulungu molimba mtima.+