Machitidwe 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Petulo atathedwa nzeru chifukwa chosamvetsa tanthauzo la masomphenya amene anaonawo, amuna otumidwa ndi Koneliyo aja anali atafunsira kuti nyumba ya Simoni ili kuti ndipo anali ataima pachipata.+
17 Petulo atathedwa nzeru chifukwa chosamvetsa tanthauzo la masomphenya amene anaonawo, amuna otumidwa ndi Koneliyo aja anali atafunsira kuti nyumba ya Simoni ili kuti ndipo anali ataima pachipata.+