Machitidwe 2:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Anali kutamanda Mulungu ndipo anthu onse anali kuwakonda.+ Komanso tsiku ndi tsiku, Yehova anapitiriza kuwawonjezera+ anthu amene anali kuwapulumutsa.+ Machitidwe 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Onse okhala mu Luda ndi m’chigwa cha Sharoni+ anamuona, ndipo anatembenukira kwa Ambuye.+
47 Anali kutamanda Mulungu ndipo anthu onse anali kuwakonda.+ Komanso tsiku ndi tsiku, Yehova anapitiriza kuwawonjezera+ anthu amene anali kuwapulumutsa.+