Machitidwe 2:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Anali kutamanda Mulungu ndipo anthu onse anali kuwakonda.+ Komanso tsiku ndi tsiku, Yehova anapitiriza kuwawonjezera+ anthu amene anali kuwapulumutsa.+ Machitidwe 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma anthu ambiri amene anamvetsera mawu awo anakhulupirira,+ ndipo chiwerengero cha amuna chinakwana pafupifupi 5,000.+ Machitidwe 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso okhulupirira Ambuye anapitiriza kuwonjezeka, chifukwa amuna ndi akazi ambirimbiri anakhala ophunzira.+ Machitidwe 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pamenepo mpingo+ mu Yudeya monse, mu Galileya, ndi mu Samariya unalowa m’nyengo yamtendere, ndipo unakhala wolimba. Popeza kuti unali kuyenda moopa Yehova+ ndiponso kulimbikitsidwa ndi mzimu woyera,+ mpingowo unali kukulirakulira.
47 Anali kutamanda Mulungu ndipo anthu onse anali kuwakonda.+ Komanso tsiku ndi tsiku, Yehova anapitiriza kuwawonjezera+ anthu amene anali kuwapulumutsa.+
4 Koma anthu ambiri amene anamvetsera mawu awo anakhulupirira,+ ndipo chiwerengero cha amuna chinakwana pafupifupi 5,000.+
14 Komanso okhulupirira Ambuye anapitiriza kuwonjezeka, chifukwa amuna ndi akazi ambirimbiri anakhala ophunzira.+
31 Pamenepo mpingo+ mu Yudeya monse, mu Galileya, ndi mu Samariya unalowa m’nyengo yamtendere, ndipo unakhala wolimba. Popeza kuti unali kuyenda moopa Yehova+ ndiponso kulimbikitsidwa ndi mzimu woyera,+ mpingowo unali kukulirakulira.