Yohane 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inenso ndidzapempha Atate, ndipo adzakupatsani mthandizi wina kuti adzakhale nanu kosatha.+ Machitidwe 2:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iye anakwezedwa kudzanja lamanja la Mulungu+ ndipo analandira mzimu woyera wolonjezedwawo kuchokera kwa Atate.+ Choncho iye watitsanulira mzimu woyera umene mukuuona ndi kuumvawu.
33 Iye anakwezedwa kudzanja lamanja la Mulungu+ ndipo analandira mzimu woyera wolonjezedwawo kuchokera kwa Atate.+ Choncho iye watitsanulira mzimu woyera umene mukuuona ndi kuumvawu.