Genesis 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+ Machitidwe 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kuchokera mwa ana+ a munthu ameneyu, malinga ndi lonjezo lake, Mulungu wabweretsa mpulumutsi mu Isiraeli,+ amene ndi Yesu. Aroma 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti Abulahamu kapena mbewu yake sanalonjezedwe kuti adzalandira dziko monga cholowa chawo chifukwa cha chilamulo ayi.+ Analandira lonjezolo chifukwa chakuti anali wolungama mwa chikhulupiriro.+
3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+
23 Kuchokera mwa ana+ a munthu ameneyu, malinga ndi lonjezo lake, Mulungu wabweretsa mpulumutsi mu Isiraeli,+ amene ndi Yesu.
13 Pakuti Abulahamu kapena mbewu yake sanalonjezedwe kuti adzalandira dziko monga cholowa chawo chifukwa cha chilamulo ayi.+ Analandira lonjezolo chifukwa chakuti anali wolungama mwa chikhulupiriro.+