Machitidwe 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 chifukwa simudzasiya moyo wanga m’Manda,* ndipo simudzalola kuti thupi la wokhulupirika wanu livunde.+
27 chifukwa simudzasiya moyo wanga m’Manda,* ndipo simudzalola kuti thupi la wokhulupirika wanu livunde.+