Habakuku 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Yang’anani pakati pa mitundu ya anthu ena anthu inu, ndipo muyang’anitsitse, kenako muyang’anane modabwa.+ Dabwani pakuti pali ntchito imene winawake akuichita m’masiku anu imene anthu inu simungakhulupirire ngakhale wina atakufotokozerani.+
5 “Yang’anani pakati pa mitundu ya anthu ena anthu inu, ndipo muyang’anitsitse, kenako muyang’anane modabwa.+ Dabwani pakuti pali ntchito imene winawake akuichita m’masiku anu imene anthu inu simungakhulupirire ngakhale wina atakufotokozerani.+