Machitidwe 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma Ayuda amene sanakhulupirire, anauza zoipa+ anthu a mitundu ina ndi kupotoza maganizo awo kuti atsutsane ndi abalewo.+ Machitidwe 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Ayuda anafika kuchokera ku Antiokeya ndi ku Ikoniyo ndipo anakopa anthuwo.+ Choncho anaponya Paulo miyala ndi kumukokera kunja kwa mzindawo, poganiza kuti wafa.+
2 Koma Ayuda amene sanakhulupirire, anauza zoipa+ anthu a mitundu ina ndi kupotoza maganizo awo kuti atsutsane ndi abalewo.+
19 Ndiyeno Ayuda anafika kuchokera ku Antiokeya ndi ku Ikoniyo ndipo anakopa anthuwo.+ Choncho anaponya Paulo miyala ndi kumukokera kunja kwa mzindawo, poganiza kuti wafa.+