Machitidwe 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atafika kumeneko, mumzinda wa Salami anayamba kufalitsa mawu a Mulungu m’masunagoge a Ayuda. Iwo analinso ndi Yohane+ monga wowatumikira.
5 Atafika kumeneko, mumzinda wa Salami anayamba kufalitsa mawu a Mulungu m’masunagoge a Ayuda. Iwo analinso ndi Yohane+ monga wowatumikira.