1 Akorinto 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti Khristu sananditume+ kukabatiza anthu, koma kukalengeza uthenga wabwino, osati mwa nzeru za kulankhula,+ kuti mtengo wozunzikirapo* wa Khristu ungakhale wopanda pake.
17 Pakuti Khristu sananditume+ kukabatiza anthu, koma kukalengeza uthenga wabwino, osati mwa nzeru za kulankhula,+ kuti mtengo wozunzikirapo* wa Khristu ungakhale wopanda pake.