Machitidwe 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atafika kumeneko ndi kuona kukoma mtima kwakukulu+ kwa Mulungu, anakondwera+ ndipo anayamba kulimbikitsa onse kuti apitirize kukhala okhulupirika kwa Ambuye motsimikiza mtima.+
23 Atafika kumeneko ndi kuona kukoma mtima kwakukulu+ kwa Mulungu, anakondwera+ ndipo anayamba kulimbikitsa onse kuti apitirize kukhala okhulupirika kwa Ambuye motsimikiza mtima.+