Agalatiya 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti asanafike anthu ena ochokera kwa Yakobo,+ iye anali kudya+ limodzi ndi anthu a mitundu ina, koma anthuwo atafika, iye anadzipatula ndipo anasiya kuchitira nawo zinthu limodzi, chifukwa ankaopa+ anthu odulidwawo.+
12 Pakuti asanafike anthu ena ochokera kwa Yakobo,+ iye anali kudya+ limodzi ndi anthu a mitundu ina, koma anthuwo atafika, iye anadzipatula ndipo anasiya kuchitira nawo zinthu limodzi, chifukwa ankaopa+ anthu odulidwawo.+