Machitidwe 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Petulo atapita ku Yerusalemu, olimbikitsa mdulidwe+ anayamba kutsutsana naye.