2 Petulo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuwonjezera apo, muone kuleza mtima kwa Ambuye wathu kukhala chipulumutso, monganso mmene m’bale wathu wokondedwa Paulo anakulemberani mogwirizana ndi nzeru+ zimene anapatsidwa.+
15 Kuwonjezera apo, muone kuleza mtima kwa Ambuye wathu kukhala chipulumutso, monganso mmene m’bale wathu wokondedwa Paulo anakulemberani mogwirizana ndi nzeru+ zimene anapatsidwa.+